[Qu'ils sachent], cependant, qu'un seul jour, auprès de ton Seigneur, équivaut à mille ans de ce que vous comptez.
Ndipo ndithu tsiku limodzi kwa Mbuye wako lili ngati zaka chikwi chimodzi mukawerengedwe kanu.
Ton Seigneur dit aux anges, " Je vais créer l'être humain à partir de l'argile.
" (Akumbutse) pamene Mbuye wako adanena kwa angelo: "Ine ndilenga munthu kuchokera ku dothi, (yemwe ndi Adam)."
Les gens des cités sont-ils sûrs que Notre châtiment rigoureux ne les atteindra pas le jour, pendant qu'ils s'amusent?
"Kodi anthu a m'mizinda (iyo momwe muli anthu oipa) ali ndi chitetezo cholimba kuti chilango chathu sichingawadzere usiku iwo ali mtulo?
Ne vous avons-nous pas créés d'un peu d'eau,
Kodi sitidakulengeni kuchokera ku madzi
9- Dis: "Renierez-vous [l'existence] de celui qui a créé la terre en deux jours
"Nena: "Kodi inu mukumkanira yemwe adalenga nthaka mmasiku awiri (okha)?
" Et ils t'interrogent sur la menstruation des femmes. - Dis: "C'est une incommodité.
"Ndipo (iwo) akukufunsa za kukhala malo amodzi ndi azimayi panthawi imene akusamba, auze (kuti): "Zimenezo ndizovulaza (ndiponso ndiuve).
[Mais] vous êtes très peu reconnaissants.
Koma kuyamika kwanu (kwa Yemwe adakupatsani zimenezi) nkochepa kwambiri.
Ton Seigneur dit aux anges, " Je vais créer l'être humain à partir de l'argile."
" (Akumbutse) pamene Mbuye wako adanena kwa angelo: "Ine ndilenga munthu kuchokera ku dothi, (yemwe ndi Adam)."
Si nous avions voulu, nous aurions pu envoyer à chaque communauté un avertisseur.
"Ndipo tikadafuna, tikadatuma mchenjezi wawowawo m'mudzi uliwonse, (koma tatuma Muhammad {s.a.w} kuti akhale mchenjezi wa onse).
" Il n'est pas interrogé sur ce qu'Il fait, mais ce sont eux qui devront rendre compte (de leurs actes). "
"Safunsidwa pa zimene akuchita, koma iwo adzafunsidwa.
Ainsi le matin, plus rien n'était visible en dehors de leurs demeures.
Kenako adali osaonedwanso, kupatula nyumba zawo (ndizimene zidatsalira).
Revenez-y jusqu'à ce que vous en soyez satisfait (e).
Pali Bwezerani batani kwa inu ngati sindicho kuti adzathe kuchita izo mpaka inu wokhutira ndi chifukwa.
Peut-être se rappellera-t-il ou (Me) craindra-t-il ? ils dirent: " Ô notre Seigneur, nous craignons qu'il ne nous maltraite indument ou qu'il dépasse les limites ."
" (Iwo) adati: "Mbuye wathu ndithu ife tikuopa kuti angatimbwandire kapena kutipyolera malire (tisananene kanthu)."
Ce n'est que la pure vérité).
Ina ukweli, ila inauma!
Et sur la terre il y a des Signes pour ceux qui ont la certitude de la foi,
M'nthaka muli zizindikiro kwa Otsimikiza, (Zosonyeza kuti Mulungu alipo).
Ainsi en sera-t-il de tous ceux qui se font les serviteurs des sens.
Ndithu m'zimenezo muli malingaliro kwa kapolo aliyense wotembenukira (kwa Allah).
"pour celui d'entre vous qui veut suivre le chemin droit.
"Kwa yemwe mwa inu akufuna kuyenda mu njira yoongoka.
et leurs prières, s'associeront à sa peine.
Mapemphero awo amangokhala amwambo ndipo amasiya kucheza ndi olambira anzawo.
Dans tout cela il y a des signes pour tout homme plein d'endurance et de reconnaissance."
Ndithu m'zimenezo muli zizindikiro kwa yense wopirira, wothokoza.
afin que, si l'une oublie, l'autre puisse rappeler le fait.."
..." kuti ngati mmodzi mwa iwo (akazi awiriwo) angaiwale mmodzi wawo akumbutse winayo...."
"Avant, c'était lui (Kadhafi) et le peuple était faible.
Ndipo Firiaun ndi amene adalipo iye Asadabadwe, ndi khamu la anthu amidzi Yotembenuzidwa (anthu a Luti) adadza Ndi machimo (akulu).
Et il y avait dans la ville un groupe de neuf personnes qui semaient le désordre sur la terre et ne se rétablissaient pas.
"Ndipo m'mudzimo adalipo anthu asanu ndi anayi omwe amaononga pa dziko, ndipo samakonza (chilichonse koma kuchiononga).
Et Notre Seigneur le Tout Miséricordieux, c'est Lui dont le secours est imploré contre vos assertions" (18).
"Ndipo Mbuye wathu ndi (Allah) Wachifundo chambiri; Wopemphedwa chithandizo pa zimene mukusimbazo."
[11:103] Ceci devrait être une leçon pour ceux qui craignent le châtiment de l'Au-delà.
"Ndithu m'zimenezi muli lingaliro kwa yemwe akuopa chilango cha tsiku lachimaliziro.
Jeanne et d'autres croyantes ont fait pour leur Seigneur ce qu'elles ont pu.
Jowana ndi akazi ena okhulupirika ankachita zimene akanatha pothandiza Ambuye wawo
Agrandissez-les au fur et à mesure.
Ndipo kotero muwaike iwo pansi - ndipo mochuluka kwambiri.
Il est certes parmi les injustes. "
Ndithu iye ndi m'modzi wa ochita zoipa."
Voilà ce que j'aime le président latino-américain.
Ndicho chimene ine ndimakonda za pulezidenti Latin American.
Il n'est pas de mise que ce Qur'ān puisse être inventé de la part d'un autre qu'Allah.
"Ndipo sikotheka Qur'an iyi kukhala yopekedwa, yosachokera kwa Allah (monga momwe munenera).
s [o] est satisfaite.
kotero kuti adzasangalala,
C'est Toi notre protecteur, et non pas eux.
Inu ndinu Mtetezi wathu, osati iwo.
Dis: " La vérité est arrivée, et le mensonge n'a pu commencer quoi que ce soit, ni le répéter. "
"Nena: "Choonadi chadza (chisilamu); ndipo chabodza (chipembedzo cha mafano) sichidzetsa zachilendo, ndiponso sichibwerera (kukhala ndi nyonga monga kale)."
Et nous avons créé l'homme et savons ce qu'est l'esprit qui entre en lui, et nous sommes plus proches de lui que [his] tonus musculaire.
Ndithu tidamulenga munthu, ndipo Ife Tikudziwa zimene mtima wake Ukumunong'oneza; ndipo Ife tili pafupi Ndi iye kuposa mtsempha wam'khosi Mwake.
[7] Mais aussi le peuple de Noé, son fils, Thamûd, Coré et d'autres.
""Monga chikhalidwe cha anthu a Nuh, Âdi, Samudi ndi anthu omwe adadza pambuyo pawo.
Eh bien ! non ! [l'Homme] n'a pas encore accompli ce que [le Seigneur] lui a ordonné.
Ayi ndithu (munthu) sanakwaniritsebe Zimene adamulamula Mbuye wake (Mulungu chingakhale Wakhala nthawi yaitali padziko Lapansi).
Montrez-moi ce qu'ils ont créé de la Terre; ou bien ont-ils une part [de gestion*] dans les cieux ?
Tandionetsani, ndimbali iti ya nthaka adalenga; kapena iwo ali ndi gawo m'thambo; (gawo lakulenga thambo?)
Le peuple des fils d'Israël est plus nombreux et plus fort que nous."
Ana a Isiraeli achuluka kwambiri ndipo ndi amphamvu kuposa ife.'
Pour tout cela, sa colère ne s'est pas détournée, et sa main est encore étendue.
Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.
Les yeux de tous s'attendent à toi, et tu leur donnes leur nourriture en son temps.
Maso a onse ayembekeza Inu; Ndipo muwapatsa cakudya cao m'nyengo zao.
et leurs descendants se maintiendront devant toi.
zidzukulu zawo zidzakhazikika pamaso panu."
Car Nous avons mis à l'épreuve ceux qui les ont précédés.
Ndipo ndithu, tidawayesa amene adalipo Patsogolo pawo.
" La vie de ce monde est pour ceux qui ne croient pas et qui se moquent des croyants.
"Moyo wa pa dziko lapansi wakometsedwa kwa amene sadakhulupirire, ndipo amawachitira chipongwe amene akhulupirira.
Président des États-Unis d'Amérique, qui est devenu 20.
Purezidenti wa United States of America, amene anakhala 20.
Vois-tu celui qui traite de [......] la Rétribution?
"Kodi wamuona yemwe akutsutsa za mphoto (ndi chiwerengero cha tsiku lachimaliziro)?
Ceux-ci, dans les Jardins, s'interrogent entre eux
" (Iwo) adzakhala m'minda (yosasimbika kukongola kwake) akufunsana wina ndi mnzake,
Et lorsqu'ils retournaient dans leurs familles, ils faisaient des blagues sur les croyants.
"Ndipo akabwerera kwa anzawo amabwerera akusangalala (ndi kunyozedwa kwa okhulupirira);
Pourtant, Steve B. n'est pas allé en prison ce jour-là.
Komabe Steve B. sanapite kundende tsiku limenelo.
et quand tu m'as rappelé auprès de toi, c'est toi qui les observais, car tu es témoin de toute chose.
Koma pamene mudanditenga, Inu ndiye mudali Muyang'aniri pa iwo; ndipo Inu ndinu Mboni ya chilichonse."
Et Allah est suffisant en tant que Défenseur.
Ndipo Allah akukwanira kukhala Mtetezi.
Le Jour où Nous susciterons un témoin de chaque communauté, il n'y aura pas d'indulgence pour les mécréants, et ils n'auront pas d'excuses à faire valoir.
"Ndipo (akumbutse za) tsiku lomwe tidzautsa mboni mu mtundu uliwonse; kenako sikudzaloledwa, kwa amene sadakhulupirire, (kupereka madandaulo) ndipo iwo sadzauzidwa kuti afunefune chiyanjo cha Allah (koma chilango basi).