I don't want to go to school.
Sindikufuna kupita kusukulu.


Where is the toilet?
Kodi cimbudzi cili kuti?

I want to sleep.
Ndifuna kugona.

Good night!
Usiku wabwino!

How old are you?
Muli ndi zaka zingati?

Burj Khalifa is currently the tallest skyscraper in the world.
Burj Khalifa ndi nyumba yaitali yosanjikizana padziko lonse lapansi.

I came yesterday.
Ndinabwela dzulo.

I'm feeling fine.
Ndili kumva bwino.

How are you feeling now?
Kodi muli kumva bwanji tsopano?

He came on this bicycle.
Anafika panjinga pano.

He is returning to this town.
Akubwela kutauni kuno.

He is inside this house.
Ali munyumba muno.

I want hot water.
Ndifuna madzi akupya.

I want cold water.
Ndifuna madzi ozizira.

We feel hungry.
Timvera njala.

She has a house.
Ali ndi nyumba.

Do you know where the hospital is?
Mukudziwako kucipatala?

I want to buy oranges.
Ndifuna kugula malalanje.

I want to buy bananas.
Ndifuna kugula nthoci.

I want to buy pineapples.
Ndifuna kugula zinanadzi.

Have the children fixed food for you?
Ana akupangilani cakudya?

Turtles don't have teeth.
Akamba alibe mano.