# bhw/2016082.xml.gz
# ny/2016082.xml.gz


(src)="1"> © 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
(trg)="1"> © 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

(src)="2"> Syap ine nefarḇaḇyan ḇa , ma inema ḇar ro fararur farkarkor Refo ḇero supswan ḇesiper sisaramperna kuker farsarser ro sne ḇemarisen .
(trg)="2"> MAGAZINI ya Nsanja ya Olonda imalemekeza Yehova Mulungu , yemwe ndi Wolamulira wa chilengedwe chonse .
(trg)="3"> Imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wakuti Ufumu wa Mulungu posachedwapa uchotsa zoipa zonse n’kusintha dziko lapansili kukhala paradaiso .

(src)="3"> Wamarisen buk farsarser ido , mam ro www.jw.org / bhw .
(trg)="6"> Mfundo zake zimachokera m’Baibulo .
(trg)="7"> Magaziniyi sitigulitsa .

(src)="4"> Mnuk ḇeḇeyun ro syap Ibrani sefararwei wosna ro Kitab Suci Terjemahan Dunia Baru , ma sapna kada , oroba ido mnuk ḇeḇeyun ro syap Yunani sunna ro ḆAḆEASAS BABO Wos Ḇyak ro Rasras .
(trg)="9"> Ngati mukufuna kupereka ndalama zothandizira pa ntchito yolalikira pitani pa www.jw.org .
(trg)="10"> Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika , kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina .

# bhw/2016084.xml.gz
# ny/2016084.xml.gz


(src)="1"> AWAWOS ḆEPON YA
(trg)="1"> NKHANI YA PACHIKUTO

(src)="2"> ” Allah ifawi roi ḇepyum kaku ḇeko . . . .
(src)="3"> Wakanes . . . ker . . . awer . ”
(trg)="2"> “ Ayi ndithu musalire , Mulungutu ndi amene akudziwa bwino za imfayi . ”

(src)="4"> Wos nane siwos fasis ro kneram ḇin oso ḇenir ḇe Bebe .
(src)="5"> Fafisu ya isya ro karamram kma ḇyedi , ḇemar snar kecelakaan oto .
(trg)="3"> Mawuwa anayankhula ndi mayi wina pofuna kutonthoza mnzake dzina lake Bebe , yemwe bambo ake anamwalira pa ngozi ya galimoto .

(src)="6"> Bebe fyanam kaku kuker kmari .
(trg)="4"> Bebe ankagwirizana kwambiri ndi bambo ake .

(src)="7"> Karier ma bati ḇyesi sḇuk wos sneprei ḇe i , ḇape Bebe ḇyabir wos sena nḇuk sneprei ḇe i ḇa boi nafrurfa ḇyesneso .
(trg)="5"> Koma anakhumudwa kwambiri chifukwa , kwa iyeyo zinali ngati mnzakeyo akungomutsutsula pabala .

(src)="8"> Dawos ro mankundi bo ikofen , ” Marmar ḇyedi iso roi ḇepyum ḇaḇeri . ”
(trg)="6"> Bebe ankangokhalira kunena kuti , “ Si zoona kuti pali chabwino chilichonse ndi imfa ya bambo angayi . ”

(src)="9"> Taun - taun ḇyenande ramnai , Bebe fyas kaḇer sarisa ani ro syap oso .
(src)="10"> Ro fasfas ḇyeja , nasnaibos kaku snar ḇyefafardun kaker .
(trg)="7"> Patapita zaka zambiri , Bebe analemba buku lofotokoza mmene bambo ake anafera ndipo zimene ananena m’bukuli zinasonyeza kuti pa nthawiyi anali adakali ndi chisoni .

(src)="11"> Raris komam ro Bebe i , na fasaw ḇa fa snonkaku oso imnai ro fafardun ḇyedi , iḇye syadiwer rofyor snonkaku ḇemar kwar ani iso snonkaku iswar kaku .
(trg)="8"> Zimene zinachitikira Bebe zikusonyeza kuti munthu akhoza kukhala ndi chisoni kwa nthawi yaitali , makamaka ngati womwalirayo ankagwirizana naye kwambiri .

(src)="12"> Ro Refo , marmarya sapna ḇe ” mbroḇ ḇepupes ” .
(trg)="9"> Mpake kuti Baibulo limati imfa ndi “ mdani womalizira . ”

(src)="13"> ( 1 Korintus 15 : 26 ) Pok fa kokandenbur marmar ya ḇa , ma bisa fa nḇejadi ro fafisu nakam ma dun bur snonkaku koswar kaku sya .
(trg)="10"> Kunena zoona , imfa imasokoneza zinthu zambiri makamaka ngati sitimayembekezera kuti munthuyo angamwalire .

(src)="14"> Inja kaku ya ine nafrur fa na koḇefafardun ma kofawi ḇa rariso kokren buro marmarya ma roi ḇeḇewari ya .
(trg)="11"> Ndipo imfa ndi yosazolowereka .
(trg)="12"> N’chifukwa chake imfa imathetsa nzeru anthu ambiri omwe aferedwa , moti nthawi zina amakhalabe ndi chisoni kwa nthawi yaitali .

(src)="15"> Imbude na wakara : ’ Fafisu risai sne ḇefafardun ine na ḇyenande ?
(trg)="13"> Koma mwina mumadzifunsa kuti : ‘ Kodi zimatenga nthawi yaitali bwanji kuti chisoni chithe ?

(src)="16"> Rariso snonkaku oso na ifrur mnis fafardun ḇyedi ?
(trg)="14"> Kodi munthu angatani kuti apirire imfa ya munthu amene ankamukonda ?

(src)="17"> Rariso na yaḇuk sneprei ḇe snonkaku ḇefafardun sya ?
(trg)="15"> Nanga ndingatonthoze bwanji anthu amene ali ndi chisoni ?

(src)="18"> Saneraro ḇepyum isya faro snonkaku koswar ḇemar kwar sya ke ? ’
(trg)="16"> Kodi anthu amene anamwalira angadzakhalenso ndi moyo ? ’

# bhw/2016085.xml.gz
# ny/2016085.xml.gz


(src)="1"> AWAWOS ḆEPON YA | ROFYOR SNONKAKU WASWAR KAKU OSO IMAR
(trg)="1"> NKHANI YA PACHIKUTO | KODI MUNGATANI MUNTHU YEMWE MUNKAMUKONDA AKAMWALIRA ?

(src)="2"> Ras oso ḇekandera snar wasma dafduf ke ? ­
(trg)="2"> Kodi munayamba mwavutikapo ndi ululu waukulu mutadwala kwa nthawi yochepa ?

(src)="3"> Imbude na waprei fasaw inja ḇefnder kwar fafisu ya .
(trg)="3"> N’kutheka kuti munaiwala za ululuwo chifukwa choti munachira pasanapite nthawi .

(src)="4"> Ḇape , fafardun ya imnis rariryaḇa .
(trg)="4"> Koma zimenezi n’zosiyana kwambiri ndi chisoni .

(src)="5"> Dr .
(src)="6"> Alan ­ Wolfelt fyas ro syap Healing a Spouse’s Grieving ­ Heart , ” Roi oso ḇaḇeri na ’ ḇefrur mnai ’ fafardun ya .
(trg)="5"> Munthu wina dzina lake Alan Wolfelt analemba m’buku lake kuti , “ Si zoona kuti chisoni cha munthu yemwe m’bale wake wamwalira ‘ chimatha mwamsanga . ’ ”

(src)="7"> Ḇape ­ orasya ḇyenande ma kuker sansonem ro kina ma ḇesesya , fafardun ya nari napromes . ”
(trg)="6"> ( Healing a Spouse’s Grieving Heart ) Iye ananenanso kuti : “ Chisoni chimachepa pakapita nthawi komanso anthu ena akamakuthandiza . ”

(src)="8"> Imnis raris , wawasen kada rosai ḇeḇejadi ro ­ patriark Abraham i rofyor swari ryoburi .
(trg)="7"> Mwachitsanzo , taganizirani mmene Abulahamu anamvera mkazi wake atamwalira .

(src)="9"> Ro ­ fasfas Refo ḇeknam kaku ya , ikofen snar ­ ” Abraham ­ ḇyerak fa ḇyefafardun ma kyanes Sara i . ”
(trg)="8"> Baibulo limanena kuti , “ Abulahamu anayamba kumulira Sara . ”

(src)="10"> Wos ” ḇyerak fa ” kyurfasna fyandun oras fa iprei ro ­ fafardun ya .
(trg)="9"> Mawu akuti “ anayamba , ” akusonyeza kuti Abulahamu anakhalabe ndi chisoni kwa nthawi yaitali .

(src)="11"> * Contoh ḇese iso Yakub i , sankar i ­ fa ikyar snar romawa ḇyedi Yusuf i aiwan ḇeyan ḇepek oso myuni fa imar .
(trg)="10"> * Chitsanzo china ndi cha Yakobo yemwe anapusitsidwa ndi ana ake kuti Yosefe wadyedwa ndi chilombo .

(src)="12"> Ḇyefafardun ” fafisu ras ḇe ras ” , ma kina ḇyesi jadiḇa fa sḇuk sneprei ḇe i .
(trg)="11"> Yakobo anamulira mwana wake kwa “ masiku ambiri ” ndipo ana ake onse anakanika kumutonthoza .

(src)="13"> Taun ḇeḇeso ramnai , marmar Yusuf ḇyedi pok fa ḇyefnderna ḇa . ​ — Kejadian 23 : 2 ; 37 : 34 , 35 ; 42 : 36 ; 45 : 28 .
(trg)="12"> Patapita zaka zambiri Yakobo ankavutikabe ndi chisoni chifukwa cha imfa ya mwana wakeyu . — Genesis 37 : 34 , 35 ; 42 : 36 ; 45 : 28 .

(src)="14"> Rarirya kako ro baboine snonkaku ḇebor ­ sfafardun snar snonkaku sfanam si srobur si .
(trg)="14"> Masiku anonso anthu ambiri amavutika ndi chisoni kwa nthawi yaitali munthu amene ankamukonda akamwalira .

(src)="15"> Kwarapan contoh risuru ine .
(trg)="15"> Tiyeni tione zitsanzo za anthu angapo .

(src)="16"> ” Snonswa ayedi , Robert i , imar ro 9 Juli 2008 .
(trg)="16"> Mayi wina dzina lake Gail , yemwe panopa ali ndi zaka 60 , anati : “ Mwamuna wanga Robert , anamwalira pa 9 July , mu 2008 , atachita ngozi .

(src)="17"> Ro arwo fafisu roi ḇemun ḇeḇekuri ya , imnis kuker ras - ras ḇesena .
(trg)="17"> Patsikuli zinthu zinali bwinobwino ngati mmene zinkakhalira masiku onse .

(src)="18"> Rofyor rya fa fyararur ḇaime ­ nunan ro arwo ya ramnai , nusyum yaye nu , nufor nu , ma nukofen ’ yaswar au ’ .
(trg)="18"> Titamaliza kudya chakudya cham’mawa tinatsanzikana ndipo ananyamuka n’kumapita kuntchito .

(src)="19"> Taun riwonem ­ ḇyenande , ḇape yaḇefafardun kaker .
(trg)="19"> Panopa padutsa zaka 6 chimwalilireni mwamuna wangayo , koma ndimaona kuti sindidzaiwala imfa yake . ”

(src)="20"> Yabor ya - ḇerari pok fa yaḇefnder Rob marmar ḇyedi ḇa . ” ​ — Gail , ḇyeumur 60 .
(trg)="20"> Bambo wina wazaka 84 dzina lake Etienne , anati : “ Ngakhale kuti panopa padutsa zaka 18 chimwalilireni mkazi wanga , ndidakali ndi chisoni chachikulu chifukwa cha imfa yake .

(src)="21"> ” Yemir ro taun ri 18 kwar kuker binswa ayedi ḇa , ḇape yamander kaker i ma yaḇefafardun snar ryobur aya .
(trg)="21"> Ndikaona chinachake chosangalatsa m’chilengedwe , ndimayamba kumukumbukira ndipo ndimaganizira mmene akanasangalalira kuona zinthu ngati zimenezi . ”

(src)="22"> Fafisu yamam moḇ ḇepyum ido na yaswarepen ḇeri ḇe i , ma yawasen na imarisen kaku fa myam rosai yamam na . ” ​ — Etienne , ḇyeumur 84 .
(trg)="22"> Choncho , sikulakwa kumva chisoni kwa nthawi yaitali chifukwa cha imfa ya munthu amene tinkamukonda .

(src)="23"> Inja ḇaḇesneso ma sneḇaḇir ḇeradirya inema sneḇaḇir ro snonkaku ḇaken saprop dirya .
(trg)="23"> Ndipo n’zimene zimachitikira anthu ambiri .

(src)="24"> Snonkaku oser - oser fyasna fafardun ḇyedi kuker nyan ḇeḇese faro roi ḇeḇyeḇa ḇekur si , ma ipyumḇa fa koḇemankara si .
(trg)="24"> Tisaiwalenso kuti anthu amasonyeza chisoni mosiyanasiyana , ndiye kungakhale kulakwa kudzudzula munthu chifukwa cha mmene akusonyezera chisoni .

(src)="25"> Mankun ko kako , na pok fa koḇuk sasar ya ḇe mankun ko awer rofyor koḇaḇir koḇefafardun fafaya ḇa .
(trg)="25"> Komanso tisamadziimbe mlandu poganiza kuti tili ndi chisoni chopitirira malire .

(src)="26"> Rariso na kofrur mnis fafardun koḇena rai ?
(trg)="26"> Komano n’chiyani chomwe chingatithandize pa nthawi yomwe tili ndi chisoni ?

(src)="27"> Abraham romawa ḇyedi Isak i kako ḇyefafardun kawan kaku .
(trg)="27"> Isaki , yemwe anali mwana wa Abulahamu anavutikanso ndi chisoni kwa nthawi yaitali mayi ake atamwalira .

(src)="28"> Raris ḇeḇefas ro artikel “ Tirulah Iman Mereka ” ro syap ine , awin ḇyedi Sara i imar ro swaf taun rikyor kwar ḇape Isak ḇyefafardun kaker . ​ — Kejadian 24 : 67 .
(trg)="28"> Monga tafotokozera m’nkhani yakuti , “ Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo ” yomwe ili m’magaziniyi , iye ankamvabe chisoni ngakhale kuti panali patatha zaka zitatu . — Genesis 24 : 67 .

# bhw/2016086.xml.gz
# ny/2016086.xml.gz


(src)="1"> AWAWOS ḆEPON YA | ROFYOR SNONKAKU WASWAR KAKU OSO IMAR
(trg)="1"> NKHANI YA PACHIKUTO | KODI MUNGATANI MUNTHU YEMWE MUNKAMUKONDA AKAMWALIRA ?

(src)="2"> Farkankin nabor naisya kuker roi ine .
(trg)="2"> Pali malangizo osiyanasiyana okhudza zimene anthu angachite ngati ali ndi chisoni .

(src)="3"> Ḇape nakam - ḇa nefainda .
(trg)="3"> Komabe , sikuti malangizo onse amene amaperekedwa amakhala othandiza .

(src)="4"> Imnis raris ono sisya sikofen ḇe au fa wakanes ker awer ḇaido wafasna sneḇaḇir bedi kuker nyan sairiryakam awer .
(trg)="4"> Mwachitsanzo , mukakhala ndi chisoni anthu ena angakuuzeni kuti musalire komanso musasonyeze mmene mukumvera .

(src)="5"> Ono ḇese imbude sedif au fa wafrur roi ḇeḇese ma fasna sneḇaḇir bedi monda .
(trg)="5"> Pomwe ena angakukakamizeni kuti mulire komanso muchite zinthu zosonyeza kuti muli ndi chisoni .

(src)="6"> Refo ḇyuk mamam ḇemnis kaku kuker roi ine , ma fawawi dunya ro baboine nesonem na .
(trg)="6"> Baibulo lili ndi malangizo othandiza kwambiri pa nkhaniyi , omwenso akugwirizana kwambiri ndi zimene ochita kafukufuku anapeza .

(src)="7"> Ro kebudayaan ḇeḇeso skara ḇo sobe ipyumḇa fa snon sya skanes .
(trg)="7"> Anthu a zikhalidwe zina amanena kuti mwamuna salira .

(src)="8"> Ḇape kaku ya , fandun fa komai fa kokanes , syadiwer ro ḇarpon kawasa sya ke ?
(trg)="8"> Komabe sitiyenera kuchita manyazi ndi kulira ngakhale patakhala pagulu .

(src)="9"> Snonkaku ḇena fawawi ro kesehatan mental sikofenḇadir snar kankanes ima roi snonkaku sya na sifrurna rofyor sfafardun .
(trg)="9"> Akatswiri a maganizo amanena kuti sikulakwa kulira mogwetsa misozi pofuna kusonyeza chisoni .

(src)="10"> Ma fasna fafardun ro fafisu ya , na nafnoḇek au fa wasambraḇ pdef ro ḇaḇesneso bedi .
(trg)="10"> Ndipo kusonyeza chisoni kungathandize kuti pakapita nthawi muyambenso kukhala osangalala , ngakhale kuti imfa ndi yowawa .

(src)="11"> Imbape , koḇensewar fa kodwarek sneḇefafardun na nun samswen syadi .
(trg)="11"> Koma munthu amene amayesa kubisa chisoni chake amavutika kwambiri .

(src)="12"> Refo ikofenḇadirḇa snar sasar ḇaido ipyumḇa fa kokanes rofyor kofafardun .
(trg)="12"> Baibulo silinena kuti kulira n’kulakwa kapenanso kuti mwamuna sayenera kulira .

(src)="13"> Kwarapan contoh ro Yesus i .
(trg)="13"> Chitsanzo pa nkhaniyi ndi Yesu .

(src)="14"> Nya samambraḇ fa ḇyawes kaḇer snonkaku ḇemar sya , ḇape Yesus kyanes ro ḇarpon kawasa sya rofyor bati ḇyedi Lazarus imar ! ​ — Yohanes 11 : 33 - ​ 35 .
(trg)="14"> Lazaro yemwe anali mnzake wapamtima atamwalira , Yesu analira ngakhale kuti ankadziwa kuti ali ndi mphamvu zoukitsa akufa . — Yohane 11 : 33 - 35 .

(src)="15"> Na snonkaku sya simsor rofyor sefafardun snar snonkaku siswar kaku imar ro fafisu skara ḇa .
(trg)="15"> Nthawi zambiri anthu amene wachibale wawo wamwalira mwadzidzidzi , amakwiya kwambiri .

(src)="16"> Roi nabor naisya ḇefrur fa snonkaku ḇefafardun sya simsor , imnis raris srower wos ḇepyum ḇa ro snonkaku sesyowi sya .
(trg)="16"> Iwo angakwiye pazifukwa zosiyanasiyana ndipo nthawi zina chingakhale chifukwa choti munthu yemwe akumudalira wanena zinazake zokhumudwitsa kapenanso zopanda umboni .

(src)="17"> Snon Afrika Selatan oso ḇenir ḇe Mike ikofen , ” Yaḇeumur 14 taun rofyor Kamam yedi ryoe .
(src)="18"> Rofyor imḇe sikram i , pendeta Anglikan ikofen snar Allah fyandun snonkaku ḇepyum ma dun fasaw si .
(trg)="17"> Mwachitsanzo , bambo wina wa ku South Africa dzina lake Mike ananena kuti , “ Bambo anga anamwalira ndili ndi zaka 14 zokha , ndipo pa maliro awo m’busa wina wa Anglican ananena kuti Mulungu amafuna anthu abwino ndipo amawatenga msanga asanakalambe .

(src)="19"> * Wos ine nafrur fa yamsor kaku snar nkofandun kaker Kamam nkoḇedi .
(trg)="18"> * Zimenezi zinandikwiyitsa koopsa chifukwa pa nthawiyi nafenso tinkawafuna kwambiri bambo athuwo .

(src)="20"> Kirine , swaf taun ri 63 ḇyenande kwar mḇoi yaḇesneso kaker . ”
(trg)="19"> Panopa patha zaka 63 koma zimandipwetekabe . ”

(src)="22"> Rofyor snonkaku siswar ya imar kanandor si , snonkaku oso na kyara , ’ Yafrur roi oso kada roi ine na ndariryaḇa ’ .
(trg)="20"> Nthawi zina anthu enanso amadziimba mlandu wachibale akamwalira mwadzidzidzi .

(src)="23"> Ḇaido swaf ḇepupes ya imbude muwawosyaye mu .
(trg)="21"> Mwinanso anganene kuti , ‘ Munthuyutu sakanamwalira ndikanachita zakutizakuti . ’

(src)="24"> Ine na nafrur fa wafafko rawo sne ḇedi ḇyuk sasarya ḇe mankundaw .
(trg)="22"> Kapenanso angadziimbe mlandu chifukwa chakuti munthuyo asanamwalire anakangana naye .

(src)="25"> Rofyor masasor ma sne ḇefafko nakyarn swaruser ḇena ido , pok fa wakram na awer .
(trg)="23"> Ngati mukudziimba mlandu kapenanso kukwiya chifukwa cha imfa ya wachibale wanu , si bwino kubisa mmene mukumvera .

(src)="26"> Ipyum syadi wawos kuker ḇati oso nari ḇerower ma ḇeḇuk kakakyar ḇe au snar sneḇaḇir ḇeradine snonkaku ḇefafardun sya sḇaḇir na kako .
(trg)="24"> M’malo mwake , mungauze mnzanu yemwe angakumvetseni ndiponso sangakuimbeni mlandu chifukwa cha mmene mukumvera .

(src)="27"> Refo ḇyuk swarapepen ḇeko , ” Bati ḇekaku fyasna saswar ya ro oras nakam , ma ḇyemanḇekanaek koḇedi ro fafisu ḇesamswen . ” ​ — Amsal 17 : 17 .
(trg)="25"> Baibulo limanena kuti : “ Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse , ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto . ” — Miyambo 17 : 17 .

(src)="28"> Bati ḇepyum kaku faro snonkaku ḇefafardun oso iso Manḇeḇedaw koḇedi , Allah Yahwe I .
(trg)="26"> Yehova Mulungu , yemwe ndi Mlengi wathu angakhale bwenzi labwino kwambiri kwa munthu amene waferedwa .

(src)="29"> Wakofenḇadir roi ḇero snemun bedi faro I ro nadi snaro ” i ḇefaduru mko . ”
(trg)="27"> Choncho muyenera kupemphera kwa iye chifukwa “ amakuderani nkhawa . ”

(src)="30"> ( 1 Petrus 5 : 7 ) Ibasyadiwer , ḇyeasas snonkaku ḇefrur rarirya nari swaruser ma sneḇaḇir sena naknon snar ” saswar - ḇaḇye ro Allah , ḇesyadi ro kakara ” .
(trg)="28"> Ndipotu iye amalonjeza kuti maganizo a anthu onse omwe amapemphera kwa iye adzatsitsimulidwa ndi “ mtendere wa Mulungu umene umaposa kuganiza mozama kulikonse . ”

(src)="31"> ( Filipi 4 : ​ 6 , 7 ) Kako , iḇye kada Allah ifnoḇek au roro Wos sren ḇyedi ḇeḇuk sneprei , Refo ya .
(trg)="29"> Mulungu angakutonthozeninso kudzera m’Mawu ake , omwe ndi Baibulo .

(src)="32"> Fas mnuk - mnuk ḇeḇeso ḇeḇuk sneprei .
(trg)="30"> Mungachite bwino kupeza mavesi a m’Baibulo omwe angakutonthozeni n’kuwalemba penapake .

(src)="33"> ( Mam kotak ro baḇ ya ) .
(trg)="31"> ( Onani bokosi . )

(src)="34"> Imbude na wamarisen fa wawasen kaḇer na .
(trg)="32"> Mwinanso mungaloweze ena mwa malembawa .

(src)="35"> Wafrur rarirya na nafnoḇek au rofyor wemir ro roḇ ya ma waḇor wenef rari . ​ — ​ Yesaya 57 : 15 .
(trg)="33"> Kuganizira mfundo za m’malembawa n’kothandiza kwambiri makamaka usiku pamene muli nokha komanso tulo sitikubwera . — Yesaya 57 : 15 .

(src)="36"> Baboine , snon oso ḇeumur 40 taun oso , ḇenir ḇe Jack , binswa ḇyedi ryobur i snar dafduf kanker .
(trg)="34"> Posachedwapa , bambo wina dzina lake Jack , mkazi wake anamwalira ndi matenda a khansa .

(src)="37"> Jack ikofen ro fafisu ya myander kaku swa ḇyedi .
(trg)="35"> Jack ananena kuti nthawi zina amasowa munthu wocheza naye .

(src)="38"> Ḇape nadi ya iso ḇesambrarḇser i .
(trg)="36"> Koma amalimbikitsidwa akapemphera kwa Yehova .

(src)="39"> Ikofen , ” Rofyor yaḇenadi ḇe Yahwe I , yaḇaḇir yemirḇa .
(trg)="37"> Iye ananena kuti : “ Ndikapemphera kwa Yehova , sindionanso kuti ndili ndekha .

(src)="40"> Ro roḇ yakandor bo yakḇok ma yaḇor yenef rari .
(trg)="38"> Nthawi zambiri ndikadzidzimuka m’kati mwa usiku sindigonanso .

(src)="41"> Ḇape ro - fyor yawasya ma yawasen wos ḇero Refo ya ramnai yaḇenadi yakofen roi ḇero snemun yedi , sne yedi iprei ma iknon kaku , nafrur fa sne ma swaruser ayena naknon inja bisa fa yenef wer . ”
(trg)="39"> Zikatere ndimangotenga Baibulo n’kuyamba kuwerenga , kenako ndimaganizira zomwe ndawerengazo ndiponso kupemphera kwa Yehova .
(trg)="40"> Zimenezi zimandithandiza kuti ndiyambe kumva bwino mumtimamu ndipo tulo timabweranso . ”

(src)="42"> Inkbor oso ḇenir ḇe Vanessa snari ryoburi snaro idufe .
(trg)="41"> Chitsanzo china ndi Vanessa yemwe mayi ake anamwalira atadwala kwambiri .

(src)="43"> I kako isma samambraḇ ro nadi ya .
(trg)="42"> Nayenso anaona kuti pemphero ndi lothandiza kwambiri .

(src)="44"> Ikofen , ” Ro fafisu ḇesamswen kaku yor monda Allah snonsnon ḇyedi ma yakanes .
(trg)="43"> Vanessa ananena kuti : “ Zinthu zikafika povuta kwambiri ndinkangoyamba kupemphera n’kumatchula dzina la Mulungu kwinaku ndikulira .

(src)="45"> Yahwe ryower nadi ayena ma ḇyuk samambraḇ yafandun na ḇesya kwar . ”
(trg)="44"> Yehova ankamva mapemphero anga ndipo ankandipatsadi mphamvu . ”

(src)="46"> Psikolog sya sḇuk ananun faro snonkaku ḇefafardun sya insama sifnoḇek snonkaku ḇese ḇaido sḇuk oras sena fa sfarmyan faro kawasa kam .
(trg)="45"> Anthu ena amene amakonda kulangiza anthu amene akuvutika ndi chisoni , amawauza kuti azithandiza ena kapenanso kugwira ntchito zina za m’dera lawo .

(src)="47"> Si - frur roi ine na nḇuk marasrisen ḇesi ma na napyos sne ḇefafardun sena .
(trg)="46"> Zimenezi zingathandize kuti azisangalala komanso kuti chisoni chawo chichepeko .

(src)="48"> ( Farfyar Ro Manwawansya 20 : 35 ) Snonkaku Kristen ḇebor ḇefafardun sya sisma sneprei ḇeba kaku snar sifnoḇek snonkaku ḇese sya . ​ — 2 Korintus 1 : ​ 3 , 4 .
(trg)="47"> Akhristu ambiri omwe aferedwa amayesetsa kuthandiza ena ndipo amaona kuti kuchita zimenezi kumawatonthoza kwambiri . — 2 Akorinto 1 : 3 , 4 .

(src)="49"> Inema farkarkor ḇeknam ro Refo isyaḇa .
(trg)="48"> Baibulo siliphunzitsa zimenezi .

(src)="50"> Refoya fyasnaḇadir roi ri - kyor ḇefnai marmar ya . ​ — Pengkhotbah 9 : ​ 11 ; Yohanes 8 : ​ 44 ; Roma 5 : ​ 12 .
(trg)="49"> M’malo mwake , limafotokoza zifukwa zitatu zimene zimachititsa kuti anthu azifa . — Mlaliki 9 : 11 ; Yohane 8 : 44 ; Aroma 5 : 12 .

(src)="51"> Allah ḇyaḇir ḇaḇekandera wasmana . ​ — Mazmur 55 : 22 ; 1 Petrus 5 : 7 .
(trg)="50"> Mulungu zimamukhudza kwambiri inuyo mukamavutika — Salimo 55 : 22 ; 1 Petulo 5 : 7 .