# ab/2016162.xml.gz
# nya/2016162.xml.gz


(src)="1"> © 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
(trg)="1"> © 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

(src)="2"> Бесплатно .
(trg)="6"> Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibulo .

(src)="3"> Хәыда - ԥсада .
(trg)="7"> Magazini iyi si yogulitsa .

(src)="4"> Ари аҭыжьымҭа адунеизегьтәи абиблиатә рҵаратә ус иахәҭакуп , хатәгәаԥхарала иалаҵоу аԥарала иҟоуп , насгьы Иегова ишаҳаҭцәа имҩаԥыргоит .
(trg)="8"> Colinga cake ndi kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene imacitika padziko lonse lapansi .
(trg)="9"> Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi .

(src)="6"> Егьи аиҭага : АдҾ — ацитатақәа еиҭагоуп урысшәала иҭыжьу « Иԥшьоу Аҩыра — Адунеи ҿыц аиҭага » аҟынтә
(trg)="10"> Kuti mucite copeleka , pitani pa webusati ya www.jw.org .
(trg)="11"> Baibulo limene taseŵenzetsa ndi Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa lina .

# ab/2016163.xml.gz
# nya/2016163.xml.gz


(src)="1"> АЦӘА́ АҞЫНТӘ ИААГОУ АТЕМА | ИЗБАН ХРИСТОС ДЫЗГӘАҞЫЗ , НАСГЬЫ ДЗЫԤСЫЗ ?
(trg)="1"> NKHANI YA PACIKUTO | N’CIFUKWA CIANI YESU ANAVUTIKA NDI KUTIFELA ?

(src)="2"> Ааԥынра 33 шықәса ҳ . ҳ .
(trg)="2"> Mu 33 C.E . , Yesu wa ku Nazareti anaphedwa .

(src)="3"> Назареттәи Иисус дкыдҵаны дшьын .
(trg)="3"> Iye anapatsidwa mlandu wabodza woukila boma , anamenyedwa mwankhanza , ndipo anakhomeledwa pamtengo .

(src)="5"> Иара ӷәӷәала дгәаҟны дыԥсит .
(trg)="4"> Iye anafa imfa yoŵaŵa .

(src)="6"> Аха Анцәа Иисус иԥсы ҭеиҵеит , насгьы 40 мшы рышьҭахь иара ажәҩан ахь дцеит .
(trg)="5"> Koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa , ndipo patapita masiku 40 Yesu anabwelela kumwamba .

(src)="7"> Ари ажәабжь Аевангелиақәа ԥшьба рҟны иануп , урҭ Ақьырсиан Бырзен Ҩырақәа ( ма Ауасиаҭ Ҿыц ) ирыхәҭакуп .
(trg)="6"> Zocitika zapadela zimenezi zinalembedwa m’mabuku anai a Uthenga Wabwino a m’Malemba Acigiliki Acikristu , amene amadziŵika kuti Cipangano Catsopano .

(src)="8"> Иҟалаҵәҟьазма урҭ ахҭысқәа ?
(trg)="7"> Kodi zimene zinalembedwa m’mauthenga amenewo zinacitikadi ?

(src)="9"> Ари азҵаара хшыҩзышьҭрала иазнеитәуп .
(trg)="8"> Funso limeneli n’lofunika kwambili .

(src)="10"> Уи хыҭҳәаазар , ақьырсиантә гәрахаҵара ҵакыдоуп , насгьы џьанаҭ дгьыл аҿы наӡаӡатәи аԥсҭазааразы агәыӷра инамӡоу гәыхәтәуп ( 1 Коринфаа рахь 15 : 14 ) .
(trg)="9"> Ngati zinthu zimenezo sizinacitike , ndiye kuti cikhulupililo ca Akristu n’copanda nchito , ndipo ciyembekezo cokhala ndi moyo m’Paladaiso ndi loto cabe .
(trg)="10"> ( 1 Akorinto 15 : 14 ) Komabe , ngati zinthuzo zinacitikadi , ndiye kuti anthu ali ndi tsogolo labwino kwambili , limene inu mungauzeko ena .

(src)="12"> Ирнузеи нас Аевангелиақәа — аиаша , мамзаргьы ахыҭҳәаа ?
(trg)="11"> Koma kodi nkhani za m’Mauthenga Abwino zinacitika kapena sizinacitike ?

(src)="13"> Аевангелиақәа амифқәеи алегендақәеи ирыҿурԥшуазар , урҭ иааџьоушьартә ииашоуп , насгьы рацәак ихадам ахәҭақәа инҭкааны ирзааҭгылоит .
(trg)="12"> Mosiyana ndi nthano zabodza , nkhani za m’Mauthenga Abwino zinafufuzidwa mosamala ndi kulembedwa molondola .

(src)="14"> Иаҳҳәап , абиблиатә текст аҿы иануп агеографиатә ҭыԥқәа рыхьӡқәа рацәаны , урҭ рҟынтә акыр лабҿаба иубар улшоит .
(trg)="13"> Mwacitsanzo , zimachula maina a malo enieni , ndipo ambili mwa malo amenewa anthu angapite kukawaona masiku ano .

(src)="15"> Аевангелиақәа рҿы иҟаҵәҟьаз ауаа рыӡбахә аҳәоит , урҭ шыҟаҵәҟьаз аҭоурыхҭҵааҩцәагьы ишьақәдырӷәӷәоит ( Лука 3 : 1 , 2 , 23 ) .
(trg)="14"> Cina , zimafotokoza anthu enieni , ndipo akatswili olemba mbili yakale amacitila umboni kuti anthuwo analikodi . — Luka 3 : 1 , 2 , 23 .

(src)="16"> Иисус Христос иӡбахә рҳәоит актәи , насгьы аҩбатәи ашәышықәсақәа рзы инхоз ибиблиатәым авторцәа * .
(trg)="15"> Olemba ena a m’nthawi ya atumwi komanso a m’zaka za m’ma 100 C.E . , anachulapo za Yesu .
(trg)="16"> * Njila imene Yesu anaphedwela yofotokozedwa m’Mauthenga Abwino ndi yofanana ndi njila zimene Aroma anali kugwilitsila nchito pakupha munthu .

(src)="17"> Аевангелиақәа рҿы иаагоу Иисус дшыршьыз аметод усҟантәи аамҭазы Римтәи аимпериаҿы рхы иадырхәоз ашьра аметодқәа ирықәшәоит .
(trg)="17"> Kuonjezela apo , zocitika zimene analemba ndi zofanana m’njila yakuti zinalembedwa molondola ndiponso mosapita m’mbali .
(trg)="18"> Iwo analembanso ngakhale zolakwa za ophunzila ena a Yesu .

(src)="18"> Уи адагьы , ахҭысқәа еилых ҟамҵакәа , мцык аламҵакәа иануп , насгьы Иисус иҵаҩцәа ԥыҭҩык рыгхақәаҵәҟьагьы арбоуп ( Матфеи 26 : 56 ; Лука 22 : 24 — 26 ; Иоанн 18 : 10 , 11 ) .
(trg)="19"> ( Mateyu 26 : 56 ; Luka 22 : 24 - 26 ; Yohane 18 : 10 , 11 ) Maumboni onsewa akuonetsa kuti olemba Mauthenga Abwino anali oona mtima , ndipo analemba zinthu zokhudza Yesu molondola kwambili .

(src)="19"> Арҭ афакторқәа зегьы ишьақәдырӷәӷәоит аевангелистцәа Христос иԥсҭазаара аҟынтә ахҭысқәа мцык аламҵакәа , насгьы ишыҟаҵәҟьаз ишанырҵаз .
(trg)="20"> Ngakhale kuti ambili amakhulupilila kuti Yesu anabweladi padziko lapansi kenako anaphedwa , ena amakaikila zakuti iye anaukitsidwa .

(src)="20"> Аӡәырҩы ауаа агәра ргоит Иисус дшыҟаз , насгьы дшыԥсыз , аха шьоукы иԥсы шҭалаз агәра ргаӡом .
(trg)="21"> Atumwi ake naonso sanakhulupilile pamene anamva lipoti lakuti iye waukitsidwa .

(src)="21"> Апостолцәаҵәҟьагьы Иисус иԥсы ҭоуп ҳәа анрарҳәа , раԥхьа агәра рымгеит ( Лука 24 : 11 ) .
(trg)="22"> ( Luka 24 : 11 ) Komabe , pamene io ndi ophunzila ena anamuona Yesu woukitsidwayo panthawi zosiyanasiyana , m’pamene anakhulupilila .

(src)="23"> Иаҳҳәап зны иара 500 - ҩык инареиҳаны ауаа дрызцәырҵит ( 1 Коринфаа рахь 15 : 6 ) .
(trg)="23"> Ndipo panthawi ina , Yesu anaonekela kwa anthu oposa 500 . — 1 Akorinto 15 : 6 .

(src)="24"> Иисус иҵаҩцәа рхақәиҭреи рыԥсҭазаареи ашәарҭара иҭаргыланы иԥсҭалара атәы ауаа ирзеиҭарҳәон , дызшьызгьы уахь инарылаҵаны ( Аусқәа 4 : 1 — 3 , 10 , 19 , 20 ; 5 : 27 — 32 ) .
(trg)="24"> Molimba mtima , ophunzila a Yesu analengeza za kuukitsidwa kwake kwa anthu ambili kuphatikizapo amene anamupha , ngakhale kuti kucita zimenezo kunaika moyo wao pangozi .
(trg)="25"> ( Machitidwe 4 : 1 - 3 , 10 , 19 , 20 ; 5 : 27 - 32 ) Kodi ophunzila ambili akanalimba mtima conco zikanakhala kuti sanali otsimikiza mtima kuti Yesu anaukitsidwadi ?

(src)="25"> Иаадырԥшрызма ус еиԥш иҟоу агәымшәара иҵаҩцәа , иара иԥсы шҭалаз агәра рымгозҭгьы ?
(trg)="26"> Kukamba zoona , mfundo yakuti Yesu anaukitsidwadi ndi imene inacititsa kuti Cikristu cifalikile kwambili m’nthawi zakale ngakhale masiku ano .

(src)="26"> Христос иԥсҭалара афакт абзоурала ақьырсианра ари адунеи анырра ӷәӷәа анаҭоит .
(trg)="27"> Nkhani zokhudza imfa ya Yesu ndi kuukitsidwa kwake zolembedwa m’Mauthenga Abwino , ndi umboni wakuti nkhani zonse zofotokoza mbili yakale n’zoona .

(src)="28"> Урҭ Аевангелиақәа шәыхшыҩ азышьҭны шәрыԥхьозар , агәра жәгоит уа иаагоу ахҭысқәа ииашаҵәҟьаны ишыҟаз .
(trg)="28"> Kuŵelenga nkhani zimenezi bwinobwino , kudzakuthandizani kukhulupilila kuti zinacitikadi .

(src)="29"> Арҭ ахҭысқәа зыҟалаз еилышәкаар , шәыгәрахаҵара еиҳагьы иӷәӷәахоит .
(trg)="29"> Ndipo cikhulupililo canu cidzalimbanso mukamvetsetsa cifukwa cake zinthuzo zinacitika .

(src)="30"> Уи анаҩстәи астатиа ишәеилнаркаауеит .
(trg)="30"> Nkhani yotsatila ifotokoza zimenezi .

(src)="31"> Иаҳҳәап , римтәи аҭоурыхҭҵааҩ Та́цит ( диит 55 шықәса раҟара ҳ . ҳ . ) иҩит « ари ахьӡ ( ақьырсианцәа ) зхылҿиааз Христос , Тибери ихаан апрокуратор Понти Пилат иоуп дызшьыз » ҳәа .
(trg)="31"> Ena mwa anthu amenewa ndi Tacitus , amene anabadwa mu 55 C.E .

(src)="32"> Иара убас Иисус иӡбахә рҳәоит римтәи аҭоурыхҭҵааҩ Светони ( I ашәышықәса ҳ . ҳ . ) , аиудеитәи аҭоурыхҭҵааҩ Иосиф Флави ( I ашәышықәса ҳ . ҳ . ) , насгьы Плини Аиҵбы , Вифиниа анапхгаҩы ( II ашәышықәса алагамҭа ҳ . ҳ . ) .
(trg)="32"> Iye analemba kuti Akristu anatengela dzinali kwa “ Kristu ” amene Pontiyo Pilato , mmodzi mwa olamulila athu , anamulamula kuti azunzidwe ndi kuphedwa mu ulamulilo wa mfumu Tiberiyo . ”
(trg)="33"> Enanso amene analemba za Yesu anali Suetonius , ( wa m’nthawi ya atumwi ) , wolemba mbili yakale waciyuda Josephus ( wa m’nthawi ya atumwi ) , ndi Pliny Wamng’ono amene anali bwanamkubwa wa ku Bituniya ( wa kumayambililo kwa zaka za m’ma 100 C.E ) .

(src)="33"> Христос ауаатәыҩса ириҭаз анырра ӷәӷәа уазхәыцуазар , иазыԥштәума иара и́ҟазаареи иԥсҭалареи шьақәзырӷәӷәо ибиблиатәым ахыҵхырҭақәа еиҳаны иԥшаахоит ҳәа ?
(trg)="34"> Ponena za mmene zocita za Yesu zinakhudzila anthu padziko lapansi , kodi tingayembekezele kupeza maumboni ena a m’nthawi ya atumwi kuposa a m’Baibulo , amene akuonetsa kuti Yesu anali munthu weniweni ndi kuti anaukitsidwa ?

(src)="34"> Ус акәымхаргьы ҟалоит .
(trg)="35"> Osati kwenikweni .

(src)="35"> Акы , Аевангелиеқәа 2 000 шықәса раҟара раԥхьа иҩын .
(trg)="36"> Coyamba , Mauthenga Abwino analembedwa zaka pafupifupi 2,000 zapitazo .
(trg)="37"> Ndipo zolemba zina za m’nthawi imeneyo zikalipo .

(src)="36"> Уи аамҭаз иҟаз егьырҭ аҩыратә хыҵхырҭақәа маҷны иаанхеит ( 1 Пиотр 1 : 24 , 25 ) .
(trg)="38"> ( 1 Petulo 1 : 24 , 25 ) Ndiyeno , anthu ambili amene anali kutsutsa Yesu sakanalemba zinthu zimene zikanapangitsa anthu kukhulupilila Yesu .

(src)="37"> Ҩбагьы , Иисус иҿагылаҩцәа иаанрыжьрымызт иара дшыҟаз иазкыз аҩыратә шьақәырӷәӷәарақәа .
(trg)="39"> Pankhani ya kuukitsidwa kwa Yesu , Petulo , amene anali mmodzi wa atumwi ake , anafotokoza kuti : “ Ameneyu Mulungu anamuukitsa tsiku lacitatu ndi kumulola kuonekela , osati kwa anthu onse , koma kwa mboni zoikidwilatu ndi Mulungu , zomwe ndi ife amene tinadya ndi kumwa naye limodzi atauka kwa akufa . ”

(src)="38"> Матфеи иҟынтә Аевангелие аҿы иануп Иисус иаӷацәа иԥсы шҭалаз анеилыркаа , уи ажәабжь ауаа ирыламҵәарц рҽазыршәеит ҳәа ( Матфеи 28 : 11 — 15 ) .
(trg)="40"> ( Machitidwe 10 : 40 , 41 ) N’cifukwa ciani sanaonekele kwa anthu onse ?
(trg)="41"> Uthenga Wabwino wa Mateyu umatiuza kuti pamene atsogoleli acipembedzo amene anali adani a Yesu anamva kuti iye waukitsidwa , io anapeza njila yothetsela kufalitsidwa kwa nkhani yakuti Yesu wauka . — Mateyu 28 : 11 - 15 .

(src)="40"> Даныбзаха , дангыла ашьҭахь Иареи ҳареи акреицаҳфон , акреицаҳжәуан » ( Аусқәа 10 : 40 , 41 ) .
(trg)="42"> Kodi izi zitanthauza kuti Yesu anali kufuna kuti nkhani yakuti iye anaukitsidwa isafalikile ?
(trg)="43"> Iyai .

(src)="41"> Иаа́нагома урҭ ажәақәа Иисус иԥсы шҭалаз ауаа ирцәиҵәахыр иҭахын ҳәа ?
(trg)="44"> Petulo anapitiliza kufotokoza kuti : “ Anatilamula kuti tilalikile kwa anthu ndi kupeleka umboni wokwanila wakuti iyeyu ndi amene Mulungu anamuika kukhala woweluza anthu amoyo ndi akufa . ”

(src)="42"> Мап , избанзар Пиотр анаҩс иҳәеит : « Уи ҳарҭ иҳадиҵеит зыԥсы ҭоугьы , иҭамгьы рықәнага ӡбаҩыс аиура Анцәа Иара инапы ишаниҵаз ауаажәлар ирылаҳарҵәаларазы , шаҳаҭцәас ҳауразы » ( Аусқәа 10 : 42 ) .
(trg)="45"> Akristu oona akhala akucita zimenezi kuyambila kale . — Machitidwe 10 : 42 .

# ab/2016164.xml.gz
# nya/2016164.xml.gz


(src)="1"> АЦӘА́ АҞЫНТӘ ИААГОУ АТЕМА
(trg)="1"> NKHANI YA PACIKUTO

(src)="2"> « Аӡәы заҵәык ихҟьаны адунеи агәнаҳа аҭааит , агәнаҳа — аԥсра ахылҿиааит » ( Римаа рахь 5 : 12 )
(trg)="2"> ‘ Ucimo unaloŵa m’dziko kudzela mwa munthu mmodzi [ Adamu ] , ndi imfa kudzela mwa ucimo . ’ — Aroma 5 : 12

(src)="3"> Ишәҭахума шәара наӡаӡа шәынхалар ?
(trg)="3"> Mungayankhe bwanji mutafunsidwa kuti , “ Kodi mungakonde kukhala ndi moyo kwamuyaya ? ”

(src)="5"> Аӡәырҩы ирыԥхьаӡоит , аԥсра – ари аԥсҭазаара иахәҭаку , узцәымцо акоуп ҳәа .
(trg)="4"> Anthu ambili angakambe kuti inde , koma amaona kuti zimenezo sizingacitike .

(src)="6"> Аха азҵаара ԥсахны ишәазҵаар : « Шәазхиоума аԥсра ? »
(trg)="5"> Iwo amakamba kuti anthufe tinalengedwa kuti tizifa .

(src)="7"> ҳәа — ишԥаҟашәҵарыз аҭак ?
(trg)="6"> Koma bwanji ngati akufunsani kuti , “ Kodi mwakonzekela kufa ? ”

(src)="9"> Иҳаилнаркаауазеи уи ?
(trg)="7"> Anthu ambili angakambe kuti iyai .

(src)="10"> Ауаа ауадаҩрақәеи арыцҳарақәеи ишрықәшәогьы аԥсра рҭахӡам .
(trg)="8"> Izi zionetsa kuti mwacibadwa anthufe timafuna kukhalabe ndi moyo , ngakhale kuti timakumana ndi mavuto ambili .

(src)="11"> Абиблиа иҳаилнаркаауеит ауаа ус еиԥш иҟоу агәазыҳәара рылазҵаз Анцәа шиакәу .
(trg)="9"> Baibulo limakamba kuti Mulungu analenga anthu ndi cifuno cokhala ndi moyo kwamuyaya .

(src)="12"> Уаҟа иануп : « Иара ауаа рыгәқәа ирҭеиҵеит наӡаӡа аҟазаара » ( Екклезиаст [ Экклезиаст ] 3 : 11 ) .
(trg)="10"> Limakamba kuti “ [ iye ] anapatsa anthu mtima wofuna kukhala ndi moyo mpaka kalekale . ” — Mlaliki 3 : 11 .

(src)="13"> Аха иахьа аӡәгьы наӡаӡа дынхаӡом .
(trg)="11"> Koma zoona zake n’zakuti anthu sakhala ndi moyo kwamuyaya .

(src)="14"> Иҟалазеи ?
(trg)="12"> Nanga n’ciani cinalakwika ?

(src)="15"> Насгьы иҟаиҵазеи Анцәа аҭагылазаашьа ириашарц азы ?
(trg)="13"> Kodi Mulungu anacitapo ciliconse kuti akonze zinthu ?

(src)="16"> Абиблиаҿы иҟоу аҭакқәа агәыӷра ҳарҭоит .
(trg)="14"> Mayankho a m’Baibulo ndi okhazika mtima pansi , ndipo amaonetsa cifukwa cake Yesu anavutika ndi kufa .

(src)="17"> Уи адагьы , урҭ аҭакқәа Иисус игәаҟреи иԥсреи зыхҟьаз амзызқәа ирыдҳәалоуп .
(trg)="15"> Macaputala atatu oyambilila a buku la Genesis m’Baibulo , amatiuza kuti Mulungu anapatsa anthu oyambilila Adamu ndi Hava mwai wakuti akhale ndi moyo kwamuyaya .

(src)="19"> Абиблиаҿы иара убас иануп ауаа Анцәа ишизымӡырҩыз , уи алшарагьы шырцәыӡыз .
(trg)="16"> Iye anawauza zimene anayenela kucita kuti akhale kwamuyaya .
(trg)="17"> Macaputala amenewa afotokoza kuti iwo sanamvele Mulungu ndipo anataya mwai umenewo .

(src)="20"> Ари аҭоурых имариоу абызшәала иҩуп , убри аҟынтә шьоукы уи лакәны ирыԥхьаӡоит .
(trg)="18"> Anthu ambili amaona kuti nkhani imeneyo ndi nthano cabe .

(src)="21"> Аха иҟоуп имаҷымкәа ашьақәырӷәӷәарақәа ашәҟәы Аҟазаара Аевангелиақәа реиԥш , мцра злам аҭоурыхтә нҵамҭоуп ҳәа * .
(trg)="19"> Koma mofanana ndi mabuku a Uthenga Wabwino , zimene zinalembedwa m’buku la Genesis ponena za mbili yakale n’zoona .
(trg)="20"> *

(src)="22"> Иахылҿиаазеи Адам иааирԥшыз азымӡырҩра ?
(trg)="21"> Kodi n’ciani cinacitika pambuyo pakuti Adamu sanamvele Mulungu ?

(src)="23"> Абиблиаҿы иануп : « Аӡәы заҵәык ихҟьаны адунеи агәнаҳа аҭааит , агәнаҳа — аԥсра ахылҿиааит , абасала , урҭ зегьы иԥсуа - ианыҵуа уааԥсырахеит , избан акәзар агәнаҳа иаҵалт » ( Римаа рахь 5 : 12 ) .
(trg)="22"> Baibulo limayankha kuti : “ Monga mmene ucimo unaloŵela m’dziko kudzela mwa munthu mmodzi [ Adamu ] ndi imfa kudzela mwa ucimo , imfayo n’kufalikila kwa anthu onse cifukwa onse anacimwa . ”

(src)="24"> Адам Анцәа дизымӡырҩӡеит , агәнаҳа ҟаиҵеит .
(trg)="23"> ( Aroma 5 : 12 ) Mwakusamvela Mulungu , Adamu anacimwa .

(src)="25"> Абасала иара ицәыӡит наӡаӡа анхара алшара , аҵыхәтәаны дыԥсит .
(trg)="24"> Zimenezi zinacititsa kuti ataye mwai wokhala ndi moyo kwamuyaya .

(src)="26"> Иара ҳаихылҵит аҟынтә , ҳара иаҳҭынхеит агәнаҳа .
(trg)="25"> Patapita nthawi , iye anafa .
(trg)="26"> Popeza ndife mbadwa zake , tinatengela ucimo kwa iye .

(src)="27"> Уи иахҟьаны ҳачмазаҩхоит , ҳажәуеит , ҳаԥсуеит .
(trg)="27"> Ndiye cifukwa cake timadwala , timakalamba , ndi kufa .

(src)="28"> Ауаа зыԥсуа иазкны Абиблиа иаҳәо аилкаареи , ашьҭамҭа иазкны иҟоу иахьатәи анаукатә дыррақәеи еиқәшәоит .
(trg)="28"> Izi n’zofanana ndi mmene mwana amatengela zocita za makolo ake .

(src)="29"> Аха иҟаиҵазеи Анцәа аҭагылазаашьа ариашаразы ?
(trg)="29"> Kodi Mulungu anacitapo ciliconse kuti akonze zinthu ?

(src)="30"> Анцәа ирхынҳәит Адам ихарала ауаа ирцәыӡыз наӡаӡа анхара алшара .
(trg)="30"> Mulungu anapanga makonzedwe akuti abwezeletse mwai wokhala ndi moyo kwamuyaya umene Adamu anataya kwa mbadwa zake .

(src)="31"> Ишԥаҟаиҵеи уи ?
(trg)="31"> Kodi Mulungu anacita bwanji zimenezo ?

(src)="32"> Римаа рахь 6 : 23 аҿы иануп : « Избан акәзар агәнаҳарақәа рылҵшьас , шьаугас ирзыҟоу аԥсроуп » .
(trg)="32"> M’Baibulo , pa Aroma 6 : 23 pamati : “ Malipilo a ucimo ndi imfa . ”

(src)="33"> Уи иаа́нагоит аԥсра — ари агәнаҳа алҵшәа шакәу .
(trg)="33"> Zimenezi zitanthauza kuti ucimo umabweletsa imfa .

(src)="34"> Адам агәнаҳа ҟаиҵеит , убри азы дыԥсит .
(trg)="34"> Adamu anacimwa , ndiye cifukwa cake anafa .

(src)="35"> Ҳара уи ихылҵыз ҳауп , убри аҟынтә агәнаҳа ҟаҳҵоит , уи иахылҿиаауеит аԥсра .
(trg)="35"> Mofananamo , ifenso ndife ocimwa ndipo timalandila malipilo a ucimo amene ndi imfa .

(src)="36"> Аха уи ҳара иаҳхарам , избанзар агәнаҳа шҳамаз ҳиит .
(trg)="36"> Conco , timabadwa ndi ucimo ngakhale kuti si mwakufuna kwathu .

(src)="37"> Анцәа абзиабара аарԥшны Иԥа Иисус Христос даҳзааишьҭит « агәнаҳарақәа » рҟынтә ҳҿихырц азы .
(trg)="37"> Mwacikondi , Mulungu anatuma Mwana wake , Yesu , kudzatilipilila “ malipilo a ucimo . ”

(src)="38"> Ҟалашьас иамази уи ?
(trg)="38"> Kodi zimenezi zinatheka bwanji ?

(src)="39"> Иисус иԥсра иаанартуеит насыԥ змоу , инымҵәаӡо аԥсҭазаарахь амҩа
(trg)="39"> Imfa ya Yesu inatsegula njila yodzakhala ndi moyo wacimwemwe komanso wamuyaya

(src)="40"> Агәнаҳареи аԥсреи инаӡаз Адам иҟынтә иҳауит , убри аҟынтә даҭахын даҽаӡәы инаӡаз ауаҩы Анцәа иахь дыԥсаанӡа аӡырҩра аарԥшны уи агәнаҳа аҟынтә ҳҿызхшаз .
(trg)="40"> Popeza munthu mmodzi wangwilo , Adamu , anabweletsa ucimo ndi imfa mwa kusamvela Mulungu , panafunikanso munthu wangwilo womvela mpaka imfa n’colinga cakuti atimasule ku ucimo .

(src)="41"> Абар Абиблиа уи шҳаилнаркаауа : « Аӡә иааирԥшыз азымӡырҩра иахҟьаны , ауаа рацәа агәнаҳа иаҵалазар , даҽаӡә иҟаиҵаз аӡырҩра иабзоураны , ауаа рацәа рыгәнаҳа рхыххоит » ( Римаа рахь 5 : 19 ) .
(trg)="41"> Baibulo limafotokoza kuti : “ Monga mwa kusamvela kwa munthu mmodziyo , ambili anakhala ocimwa , momwemonso kudzela mwa kumvela kwa munthu mmodziyu , ambili adzakhala olungama . ”
(trg)="42"> ( Aroma 5 : 19 ) “ Munthu mmodziyu , ” ndi Yesu .

(src)="42"> Уи аӡырҩра аазырԥшыз « Аӡәы » Иисус иакәын .
(trg)="43"> Iye anacoka kumwamba , ndi kukhala munthu wangwilo * , kenako anatifela .

(src)="44"> Уи абзоурала ҳара иҳалшоит Анцәа иҿаԥхьа иашарыла анхара , насгьы наӡаӡатәи аԥсҭазаара аиура .
(trg)="44"> Pa cifukwa cimeneci , zinakhala zotheka kwa ife kuyesedwa olungama ndi kuima pamaso pa Mulungu , komanso kukhala ndi mwai wodzakhala ndi moyo kwamuyaya .

(src)="45"> Изаҭаххазеи Иисус иԥсра ?
(trg)="45"> Nanga n’cifukwa ciani Yesu anafunika kufa ?

(src)="46"> Илымшаӡози Зегьзымчу Анцәа Адам ихылҵыз зегьы наӡаӡа анхара алшара рыҭара ?
(trg)="46"> Kodi Mulungu Wamphamvuyonse sakanangopeleka lamulo lakuti mbadwa za Adamu zikhale kwamuyaya ?

(src)="47"> Ҳәарада иара имоуп уи азы амч .
(trg)="47"> Iye anali ndi mphamvu yocita zimenezo .